Danieli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya, amene sangasinthidwe.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:8 Ulosi wa Danieli, ptsa. 118-119
8 Ndiyeno inu mfumu khazikitsani lamulo ndipo musaine+ kuti lamulolo lisasinthe, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya, amene sangasinthidwe.”+