-
Danieli 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho anapita kwa mfumu kukaikumbutsa za lamulo limene inakhazikitsa lija. Iwo anati: “Kodi inu mfumu, si paja munasainira lamulo lonena kuti kwa masiku 30 munthu aliyense amene angapezeke akupemphera kwa mulungu kapena kwa munthu wina aliyense, kupatulapo kwa inu nokha, aponyedwe mʼdzenje la mikango?” Mfumuyo inayankha kuti: “Nkhani imeneyi ndi yodziwika bwino, mogwirizana ndi malamulo a Amedi ndi Aperisiya, amene sangasinthidwe.”+
-