Danieli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sakukumverani inu mfumu kapena kumvera lamulo limene munasainira koma akumapemphera katatu pa tsiku.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 Ulosi wa Danieli, ptsa. 119-120
13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sakukumverani inu mfumu kapena kumvera lamulo limene munasainira koma akumapemphera katatu pa tsiku.”+