Danieli 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho mfumuyo inalamula kuti abweretse Danieli. Atabwera naye anamuponya mʼdzenje la mikango.+ Koma mfumu inauza Danieli kuti: “Mulungu wako amene ukumutumikira mosalekeza akupulumutsa.” Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:16 Ulosi wa Danieli, ptsa. 120-122, 126-127 Nsanja ya Olonda,11/15/1996, tsa. 912/1/1988, tsa. 14
16 Choncho mfumuyo inalamula kuti abweretse Danieli. Atabwera naye anamuponya mʼdzenje la mikango.+ Koma mfumu inauza Danieli kuti: “Mulungu wako amene ukumutumikira mosalekeza akupulumutsa.”