Danieli 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya ndipo inakana zosangalatsa zilizonse* komanso sinathe kugona.*
18 Kenako mfumu inapita kunyumba yake yachifumu. Usiku umenewo mfumuyo inasala kudya ndipo inakana zosangalatsa zilizonse* komanso sinathe kugona.*