-
Danieli 6:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Itayandikira dzenjelo, inaitana Danieli ndi mawu achisoni. Mfumuyo inafunsa Danieli kuti: “Danieli mtumiki wa Mulungu wamoyo, kodi Mulungu wako amene umamutumikira mosalekeza wakupulumutsa kwa mikango?”
-