Danieli 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga watumiza mngelo wake kudzatseka pakamwa pa mikango+ moti sinandivulaze,+ chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse ndipo inunso mfumu sindinakulakwireni chilichonse.” Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:22 Ulosi wa Danieli, ptsa. 122-123
22 Mulungu wanga watumiza mngelo wake kudzatseka pakamwa pa mikango+ moti sinandivulaze,+ chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse ndipo inunso mfumu sindinakulakwireni chilichonse.”