Danieli 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mfumu inasangalala kwambiri ndipo inalamula kuti Danieli amutulutse mʼdzenjemo. Danieli anatulutsidwadi mʼdzenjemo ndipo sanavulale paliponse chifukwa anakhulupirira Mulungu wake.+
23 Mfumu inasangalala kwambiri ndipo inalamula kuti Danieli amutulutse mʼdzenjemo. Danieli anatulutsidwadi mʼdzenjemo ndipo sanavulale paliponse chifukwa anakhulupirira Mulungu wake.+