Danieli 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno Mfumu Dariyo inalemba makalata opita kwa anthu a mitundu yonse ndi anthu olankhula zilankhulo zosiyanasiyana okhala padziko lonse lapansi+ kuti: “Mukhale ndi mtendere wochuluka.
25 Ndiyeno Mfumu Dariyo inalemba makalata opita kwa anthu a mitundu yonse ndi anthu olankhula zilankhulo zosiyanasiyana okhala padziko lonse lapansi+ kuti: “Mukhale ndi mtendere wochuluka.