Danieli 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye amapulumutsa+ ndi kulanditsa anthu ake, ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”
27 Iye amapulumutsa+ ndi kulanditsa anthu ake, ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”