Danieli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:13 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Ulosi wa Danieli, ptsa. 145-146 Nsanja ya Olonda,2/1/1998, ptsa. 17-185/15/1988, tsa. 261/1/1988, ptsa. 10-1110/15/1986, ptsa. 5-6
13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo.
7:13 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Ulosi wa Danieli, ptsa. 145-146 Nsanja ya Olonda,2/1/1998, ptsa. 17-185/15/1988, tsa. 261/1/1988, ptsa. 10-1110/15/1986, ptsa. 5-6