Danieli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Mulungu Wamʼmwambamwamba+ ndipo idzapitiriza kuzunza oyera a Mulungu Wamkulu. Idzafuna kuti isinthe nthawi ndi lamulo ndipo oyerawo adzaperekedwa mʼmanja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri ndi hafu ya nthawi.*+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:25 Ulosi wa Danieli, ptsa. 141-144, 177 Nsanja ya Olonda,8/1/1994, tsa. 3111/1/1993, ptsa. 9-10
25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Mulungu Wamʼmwambamwamba+ ndipo idzapitiriza kuzunza oyera a Mulungu Wamkulu. Idzafuna kuti isinthe nthawi ndi lamulo ndipo oyerawo adzaperekedwa mʼmanja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri ndi hafu ya nthawi.*+