-
Danieli 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Inakula kwambiri mpaka inakafika kwa gulu lakumwamba, moti inachititsa kuti ena amʼgululi komanso nyenyezi zina zigwere padziko lapansi ndipo inazipondaponda.
-