-
Danieli 8:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kumapeto kwa ufumu wawo, zochita za anthu ochimwawo zikadzafika pachimake, mfumu yooneka mochititsa mantha ndiponso yomvetsa zinthu zovuta kumva idzayamba kulamulira.
-