Danieli 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mphamvu za mfumuyo zidzachuluka, koma si iye amene adzachititse zimenezi. Idzawononga zinthu zambiri moti idzadabwitsa anthu. Chilichonse chimene mfumuyo izidzachita chizidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 10 Nsanja ya Olonda,6/15/2012, tsa. 16 Ulosi wa Danieli, ptsa. 170, 173-176
24 Mphamvu za mfumuyo zidzachuluka, koma si iye amene adzachititse zimenezi. Idzawononga zinthu zambiri moti idzadabwitsa anthu. Chilichonse chimene mfumuyo izidzachita chizidzaiyendera bwino. Idzawononga anthu amphamvu ndi anthu oyera.+
8:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, tsa. 10 Nsanja ya Olonda,6/15/2012, tsa. 16 Ulosi wa Danieli, ptsa. 170, 173-176