Danieli 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zinthu zimene zanenedwa mʼmasomphenya zokhudza nsembe zamadzulo ndi zamʼmawa zija ndi zoona. Koma iweyo usunge masomphenyawo mwachinsinsi, chifukwa akunena zimene zidzachitike mʼtsogolo patapita masiku ambiri.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:26 Ulosi wa Danieli, ptsa. 170-171
26 Zinthu zimene zanenedwa mʼmasomphenya zokhudza nsembe zamadzulo ndi zamʼmawa zija ndi zoona. Koma iweyo usunge masomphenyawo mwachinsinsi, chifukwa akunena zimene zidzachitike mʼtsogolo patapita masiku ambiri.”+