Danieli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼchaka choyamba cha Dariyo+ mwana wa Ahasiwero, wa mtundu wa Amedi, amene anaikidwa kuti akhale mfumu ya ufumu wa Akasidi,+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:1 Ulosi wa Danieli, tsa. 181
9 Mʼchaka choyamba cha Dariyo+ mwana wa Ahasiwero, wa mtundu wa Amedi, amene anaikidwa kuti akhale mfumu ya ufumu wa Akasidi,+