Danieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula mʼdzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu ndi anthu onse amʼdziko lathu.
6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula mʼdzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu ndi anthu onse amʼdziko lathu.