Danieli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, tachita zinthu zochititsa manyazi,* mofanana ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.
8 Inu Yehova, tachita zinthu zochititsa manyazi,* mofanana ndi mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.