Danieli 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sitinamvere mawu anu, inu Yehova Mulungu wathu, chifukwa sitinatsatire malamulo anu amene munatipatsa kudzera mwa atumiki anu, aneneri.+
10 Sitinamvere mawu anu, inu Yehova Mulungu wathu, chifukwa sitinatsatire malamulo anu amene munatipatsa kudzera mwa atumiki anu, aneneri.+