Danieli 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu, amene munatulutsa anthu anu mʼdziko la Iguputo ndi dzanja lamphamvu+ nʼkuchititsa kuti dzina lanu lidziwike bwino mpaka lero,+ ife tachimwa ndipo tachita zinthu zoipa. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Ulosi wa Danieli, ptsa. 183-184
15 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu, amene munatulutsa anthu anu mʼdziko la Iguputo ndi dzanja lamphamvu+ nʼkuchititsa kuti dzina lanu lidziwike bwino mpaka lero,+ ife tachimwa ndipo tachita zinthu zoipa.