6 Thupi lake linkanyezimira ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inkawala ngati mphezi, maso ake ankaoneka ngati miyuni yamoto, manja ake komanso mapazi ake ankaoneka ngati kopa+ wonyezimira, ndipo mawu ake ankamveka ngati mawu a gulu lalikulu la anthu.