Danieli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, munthu wokondedwa* kwambiri,+ mvetsera mwatcheru mawu amene ndikufuna kukuuza. Tsopano imirira chifukwa ine ndatumidwa kwa iwe.” Atandiuza zimenezi, ndinaimirira koma ndikunjenjemera.
11 Kenako iye anandiuza kuti: “Iwe Danieli, munthu wokondedwa* kwambiri,+ mvetsera mwatcheru mawu amene ndikufuna kukuuza. Tsopano imirira chifukwa ine ndatumidwa kwa iwe.” Atandiuza zimenezi, ndinaimirira koma ndikunjenjemera.