Danieli 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya ananditsekereza kwa masiku 21. Ndiyeno Mikayeli,*+ mmodzi wa akalonga aakulu,* anabwera kudzandithandiza. Pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pomwepo pafupi ndi mafumu a Perisiya. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:13 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, ptsa. 7-87/1/1987, ptsa. 11-12 Ulosi wa Danieli, ptsa. 204-205
13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya ananditsekereza kwa masiku 21. Ndiyeno Mikayeli,*+ mmodzi wa akalonga aakulu,* anabwera kudzandithandiza. Pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pomwepo pafupi ndi mafumu a Perisiya.