Danieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndabwera kudzakuthandiza kuti umvetse zimene zidzachitikire anthu a mtundu wako mʼmasiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa ndi okhudza zimene zidzachitike mʼtsogolo.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2020, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, ptsa. 11, 21
14 Ine ndabwera kudzakuthandiza kuti umvetse zimene zidzachitikire anthu a mtundu wako mʼmasiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa ndi okhudza zimene zidzachitike mʼtsogolo.”+