Danieli 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anandiuza kuti: “Kodi ukudziwa chifukwa chake ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Ndikachoka, kalonga wa Girisi abwera. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:20 Ulosi wa Danieli, ptsa. 204-205, 208
20 Ndiyeno anandiuza kuti: “Kodi ukudziwa chifukwa chake ndabwera kwa iwe? Tsopano ndibwerera kuti ndikamenyane ndi kalonga wa Perisiya.+ Ndikachoka, kalonga wa Girisi abwera.