Danieli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komabe ndikuuza zinthu zimene zinalembedwa mʼbuku la choonadi. Palibe aliyense amene akundithandiza kwambiri pa zinthu zimenezi kupatulapo Mikayeli,+ amene ndi kalonga wanu.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:21 Ulosi wa Danieli, ptsa. 204-205, 208
21 Komabe ndikuuza zinthu zimene zinalembedwa mʼbuku la choonadi. Palibe aliyense amene akundithandiza kwambiri pa zinthu zimenezi kupatulapo Mikayeli,+ amene ndi kalonga wanu.”+