Danieli 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu imene idzabwere kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake ndipo palibe amene adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira mʼDziko Lokongola+ ndipo idzakhala ndi mphamvu zoti nʼkupha anthu ambiri. Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:16 Ulosi wa Danieli, tsa. 224
16 Mfumu imene idzabwere kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake ndipo palibe amene adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira mʼDziko Lokongola+ ndipo idzakhala ndi mphamvu zoti nʼkupha anthu ambiri.