Danieli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako mmodzi mwa angelowo anafunsa munthu amene anavala nsalu uja,+ amene anaimirira pamwamba pa madzi amumtsinjewo, kuti: “Kodi padzatenga nthawi yaitali bwanji kuti zinthu zodabwitsazi zikwaniritsidwe zonse?” Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:6 Ulosi wa Danieli, tsa. 294
6 Kenako mmodzi mwa angelowo anafunsa munthu amene anavala nsalu uja,+ amene anaimirira pamwamba pa madzi amumtsinjewo, kuti: “Kodi padzatenga nthawi yaitali bwanji kuti zinthu zodabwitsazi zikwaniritsidwe zonse?”