Hoseya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova analankhula ndi Hoseya* mwana wa Beeri mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda,+ ndiponso mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 1411/15/2005, tsa. 17
1 Yehova analankhula ndi Hoseya* mwana wa Beeri mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda,+ ndiponso mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli.