Hoseya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova atayamba kulankhula kudzera mwa Hoseya, Yehova anauza Hoseya kuti: “Pita ukakwatire mkazi amene azidzachita uhule* ndipo ukakhale ndi ana ochokera kwa hule. Chifukwa dzikoli lasiyiratu kutsatira Yehova chifukwa cha uhule.”+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2016, tsa. 27 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 1411/15/2005, ptsa. 17-19
2 Yehova atayamba kulankhula kudzera mwa Hoseya, Yehova anauza Hoseya kuti: “Pita ukakwatire mkazi amene azidzachita uhule* ndipo ukakhale ndi ana ochokera kwa hule. Chifukwa dzikoli lasiyiratu kutsatira Yehova chifukwa cha uhule.”+
1:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2016, tsa. 27 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 1411/15/2005, ptsa. 17-19