Hoseya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anauza Hoseya kuti: “Mwanayo umupatse dzina lakuti Yezereeli,* popeza kwatsala nthawi yochepa kuti ndiimbe mlandu nyumba ya Yehu+ chifukwa cha magazi amene Yezereeli anakhetsa. Ndipo ndidzathetsa ufumu wa nyumba ya Isiraeli.+
4 Ndiyeno Yehova anauza Hoseya kuti: “Mwanayo umupatse dzina lakuti Yezereeli,* popeza kwatsala nthawi yochepa kuti ndiimbe mlandu nyumba ya Yehu+ chifukwa cha magazi amene Yezereeli anakhetsa. Ndipo ndidzathetsa ufumu wa nyumba ya Isiraeli.+