Hoseya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Gomeri anakhalanso ndi pakati nʼkubereka mwana wamkazi. Ndiyeno Mulungu anauza Hoseya kuti: “Mwanayo umupatse dzina lakuti Lo-ruhama,* chifukwa sindidzachitiranso chifundo+ anthu a mʼnyumba ya Isiraeli, chifukwa ndidzawathamangitsa.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 18
6 Kenako Gomeri anakhalanso ndi pakati nʼkubereka mwana wamkazi. Ndiyeno Mulungu anauza Hoseya kuti: “Mwanayo umupatse dzina lakuti Lo-ruhama,* chifukwa sindidzachitiranso chifundo+ anthu a mʼnyumba ya Isiraeli, chifukwa ndidzawathamangitsa.+