Hoseya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ndidzachitira chifundo anthu a mʼnyumba ya Yuda+ ndipo Ine Yehova Mulungu wawo ndidzawapulumutsa.+ Sindidzawapulumutsa ndi nkhondo, uta, lupanga, mahatchi* kapenanso amuna okwera pamahatchi.”+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, ptsa. 14-1511/15/2005, tsa. 18
7 Koma ndidzachitira chifundo anthu a mʼnyumba ya Yuda+ ndipo Ine Yehova Mulungu wawo ndidzawapulumutsa.+ Sindidzawapulumutsa ndi nkhondo, uta, lupanga, mahatchi* kapenanso amuna okwera pamahatchi.”+