Hoseya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ayuda ndi Aisiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzasankha mtsogoleri mmodzi nʼkutuluka mʼdzikolo chifukwa tsiku limeneli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.”+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 15
11 Ayuda ndi Aisiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzasankha mtsogoleri mmodzi nʼkutuluka mʼdzikolo chifukwa tsiku limeneli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.”+