-
Hoseya 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Apo ayi, ndiwavula kuti akhale maliseche ngati tsiku limene anabadwa.
Ndiwachititsa kukhala ngati chipululu,
Komanso ngati dziko lopanda madzi,
Nʼkuwapangitsa kuti afe ndi ludzu.
-