Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa mayi awo amachita uhule.*+

      Mayi amene anatenga pakati nʼkuwabereka achita zinthu zochititsa manyazi+ ndipo anena kuti,

      ‘Nditsatira amuna ondikonda kwambiri+

      Ndiponso amene amandipatsa chakudya ndi madzi,

      Amandipatsanso zovala za ubweya wa nkhosa, nsalu, mafuta ndi zakumwa.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena