Hoseya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sanazindikire kuti ndine amene ndinkamupatsa mbewu,+ vinyo watsopano ndiponso mafuta.Sanazindikirenso kuti ndine amene ndinamupatsa siliva wambiri,Ndiponso golide amene anthu ankamugwiritsa ntchito polambira Baala.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 19
8 Iye sanazindikire kuti ndine amene ndinkamupatsa mbewu,+ vinyo watsopano ndiponso mafuta.Sanazindikirenso kuti ndine amene ndinamupatsa siliva wambiri,Ndiponso golide amene anthu ankamugwiritsa ntchito polambira Baala.+