Hoseya 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Choncho ndidzatembenuka nʼkulanda mbewu zanga pa nthawi yokolola.Ndidzalandanso vinyo wanga watsopano pa nthawi yopanga vinyo.+Mayiyu ndidzamulandanso zovala zanga za ubweya wa nkhosa ndiponso nsalu zanga zimene amabisira maliseche ake.
9 ‘Choncho ndidzatembenuka nʼkulanda mbewu zanga pa nthawi yokolola.Ndidzalandanso vinyo wanga watsopano pa nthawi yopanga vinyo.+Mayiyu ndidzamulandanso zovala zanga za ubweya wa nkhosa ndiponso nsalu zanga zimene amabisira maliseche ake.