Hoseya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzamuimba mlandu chifukwa cha masiku amene anapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala.+Pamene ankavala mphete* ndi zinthu zina zodzikongoletsera ndipo ankatsatira amuna omukonda kwambiri.Koma ine anandiiwala,’+ watero Yehova.
13 Ndidzamuimba mlandu chifukwa cha masiku amene anapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala.+Pamene ankavala mphete* ndi zinthu zina zodzikongoletsera ndipo ankatsatira amuna omukonda kwambiri.Koma ine anandiiwala,’+ watero Yehova.