Hoseya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindidzamulola kutchulanso mayina a zifaniziro za Baala,+Ndipo sadzakumbukiranso mayina awo.+