Hoseya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzalonjeza kukukwatira kuti ukhale wanga mpaka kalekale.Ndidzalonjeza kukukwatira motsatira chilungamo,Komanso chifukwa cha chikondi chokhulupirika ndi chifundo changa.+
19 Ndidzalonjeza kukukwatira kuti ukhale wanga mpaka kalekale.Ndidzalonjeza kukukwatira motsatira chilungamo,Komanso chifukwa cha chikondi chokhulupirika ndi chifundo changa.+