Hoseya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno dziko lapansi lidzayankha mbewu, vinyo watsopano ndi mafuta,Ndipo zimenezi zidzayankha Yezereeli.*+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 153/1/1989, tsa. 14
22 Ndiyeno dziko lapansi lidzayankha mbewu, vinyo watsopano ndi mafuta,Ndipo zimenezi zidzayankha Yezereeli.*+