Hoseya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa nthawi yaitali Aisiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe, chipilala chopatulika, efodi+ ndi zifaniziro za aterafi.*+
4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa nthawi yaitali Aisiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe, chipilala chopatulika, efodi+ ndi zifaniziro za aterafi.*+