Hoseya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani mawu a Yehova inu Aisiraeli.Yehova ali ndi mlandu ndi anthu amʼdzikoli,+Chifukwa mʼdzikoli mulibe choonadi, chikondi chokhulupirika ndipo anthu ake sadziwa Mulungu.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Tsiku la Yehova, ptsa. 57-61 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 22
4 Tamverani mawu a Yehova inu Aisiraeli.Yehova ali ndi mlandu ndi anthu amʼdzikoli,+Chifukwa mʼdzikoli mulibe choonadi, chikondi chokhulupirika ndipo anthu ake sadziwa Mulungu.+