Hoseya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nʼchifukwa chake dzikoli lidzalira maliro,+Ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu.Nyama zakutchire ndi mbalame zamumlengalenga,Ngakhalenso nsomba zamʼnyanja, zidzafa. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, tsa. 22
3 Nʼchifukwa chake dzikoli lidzalira maliro,+Ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu.Nyama zakutchire ndi mbalame zamumlengalenga,Ngakhalenso nsomba zamʼnyanja, zidzafa.