Hoseya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho mudzapunthwa masanasana.Ndipo mneneri adzapunthwa nanu limodzi ngati kuti ndi usiku. Komanso mayi anu ndidzawakhalitsa chete.*
5 Choncho mudzapunthwa masanasana.Ndipo mneneri adzapunthwa nanu limodzi ngati kuti ndi usiku. Komanso mayi anu ndidzawakhalitsa chete.*