Hoseya 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimene zidzachitikire anthuwo zidzachitikiranso ansembe.Onse ndidzawaimba mlandu chifukwa cha njira zawo,Ndipo ndidzachititsa kuti zotsatira za zochita zawo ziwabwerere.+
9 Zimene zidzachitikire anthuwo zidzachitikiranso ansembe.Onse ndidzawaimba mlandu chifukwa cha njira zawo,Ndipo ndidzachititsa kuti zotsatira za zochita zawo ziwabwerere.+