Hoseya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chiwerewere, vinyo wakale ndiponso vinyo watsopanoZimalepheretsa munthu kuchita zoyenera.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 43 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, ptsa. 4-5