Hoseya 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu anga amafunsira kwa mafano awo amtengo,Ndipo amachita zimene ndodo yawo* yawauza.Chifukwa chakuti mtima wachiwerewere umawasocheretsa,Ndiponso chifukwa cha chiwerewere chawocho, amakana kugonjera Mulungu wawo.
12 Anthu anga amafunsira kwa mafano awo amtengo,Ndipo amachita zimene ndodo yawo* yawauza.Chifukwa chakuti mtima wachiwerewere umawasocheretsa,Ndiponso chifukwa cha chiwerewere chawocho, amakana kugonjera Mulungu wawo.